Yesaya 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa tsiku limenelo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Adzalamula anthu kuti alire ndi kugwetsa misozi,+Komanso kuti amete mipala ndi kuvala ziguduli. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:12 Yesaya 1, ptsa. 237-238
12 Pa tsiku limenelo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa,Adzalamula anthu kuti alire ndi kugwetsa misozi,+Komanso kuti amete mipala ndi kuvala ziguduli.