Yesaya 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mʼmalomwake mukukondwera ndi kusangalala,Mukupha ngʼombe ndi nkhosa,Mukudya nyama ndi kumwa vinyo.+ Inu mukuti, ‘Tiyeni tidye ndi kumwa, chifukwa mawa tifa.’”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:13 Yesaya 1, ptsa. 237-238
13 Koma mʼmalomwake mukukondwera ndi kusangalala,Mukupha ngʼombe ndi nkhosa,Mukudya nyama ndi kumwa vinyo.+ Inu mukuti, ‘Tiyeni tidye ndi kumwa, chifukwa mawa tifa.’”+