Yesaya 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pita kwa Sebina,+ kapitawo woyangʼanira nyumba ya mfumu, ndipo ukamuuze kuti, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2018, tsa. 25 Yesaya 1, ptsa. 238-239
15 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Pita kwa Sebina,+ kapitawo woyangʼanira nyumba ya mfumu, ndipo ukamuuze kuti,