Yesaya 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Kodi kuno kuli wachibale wako aliyense, ndipo kodi mʼbale wako anaikidwa kuno kuti iweyo udzigobere manda kunoko?’ Iye wagoba manda ake pamalo okwera. Akudzigobera malo opumulirako* mʼthanthwe. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:16 Yesaya 1, ptsa. 238-239
16 ‘Kodi kuno kuli wachibale wako aliyense, ndipo kodi mʼbale wako anaikidwa kuno kuti iweyo udzigobere manda kunoko?’ Iye wagoba manda ake pamalo okwera. Akudzigobera malo opumulirako* mʼthanthwe.