Yesaya 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iyeyo ndidzamuveka mkanjo wako ndipo lamba wako ndidzamumanga mwamphamvu mʼchiuno mwake.+ Ulamuliro wako ndidzaupereka mʼmanja mwake ndipo iye adzakhala tate wa anthu okhala mu Yerusalemu ndi amʼnyumba ya Yuda. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:21 Yesaya 1, tsa. 240
21 Iyeyo ndidzamuveka mkanjo wako ndipo lamba wako ndidzamumanga mwamphamvu mʼchiuno mwake.+ Ulamuliro wako ndidzaupereka mʼmanja mwake ndipo iye adzakhala tate wa anthu okhala mu Yerusalemu ndi amʼnyumba ya Yuda.