Yesaya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Anthu adzapachika pa iyeyo ulemerero* wonse wa nyumba ya bambo ake, mbadwa komanso ana,* ziwiya zonse zingʼonozingʼono, ziwiya zolowa ndiponso mitsuko yonse ikuluikulu.’ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:24 Yesaya 1, ptsa. 240-243
24 Anthu adzapachika pa iyeyo ulemerero* wonse wa nyumba ya bambo ake, mbadwa komanso ana,* ziwiya zonse zingʼonozingʼono, ziwiya zolowa ndiponso mitsuko yonse ikuluikulu.’