Yesaya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mbewu za ku Sihori,* zokolola zakumtsinje wa Nailo,Zimene zinkakubweretserani ndalama, zinadutsa pamadzi ambiri,+Nʼkubweretsa phindu la anthu a mitundu ina.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:3 Yesaya 1, ptsa. 245-246
3 Mbewu za ku Sihori,* zokolola zakumtsinje wa Nailo,Zimene zinkakubweretserani ndalama, zinadutsa pamadzi ambiri,+Nʼkubweretsa phindu la anthu a mitundu ina.+