Yesaya 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi ndani waganiza kuti achitire Turo zinthu zimenezi,Mzinda umene unkaveka anthu zisoti zachifumu,Umene amalonda ake anali akalonga,Umenenso ochita malonda ake ankalemekezedwa padziko lonse lapansi?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:8 Yesaya 1, ptsa. 248-249
8 Ndi ndani waganiza kuti achitire Turo zinthu zimenezi,Mzinda umene unkaveka anthu zisoti zachifumu,Umene amalonda ake anali akalonga,Umenenso ochita malonda ake ankalemekezedwa padziko lonse lapansi?+