-
Yesaya 23:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Pamapeto pa zaka 70, Yehova adzakumbukira Turo. Mzindawo udzayambiranso kulandira malipiro ndipo udzachita uhule ndi maufumu onse apadziko lapansi.
-