Yesaya 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:1 Yesaya 1, tsa. 260 Kukambitsirana, tsa. 357
24 Taonani! Yehova akuchotsa anthu onse mʼdziko nʼkulisiya lopanda kanthu.+ Iye wawononga* dzikolo,+ nʼkubalalitsa anthu okhala mmenemo.+