Yesaya 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zidzachitika mofanana kwa aliyense: Kwa anthu ndi kwa wansembe,Kwa wantchito ndi kwa mbuye wake,Kwa wantchito wamkazi ndi kwa mbuye wake wamkazi,Kwa wogula ndi kwa wogulitsa,Kwa wobwereketsa ndi kwa wobwereka,Kwa wobwereketsa ndalama ndi kwa wobwereka ndalama.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:2 Yesaya 1, tsa. 261
2 Zidzachitika mofanana kwa aliyense: Kwa anthu ndi kwa wansembe,Kwa wantchito ndi kwa mbuye wake,Kwa wantchito wamkazi ndi kwa mbuye wake wamkazi,Kwa wogula ndi kwa wogulitsa,Kwa wobwereketsa ndi kwa wobwereka,Kwa wobwereketsa ndalama ndi kwa wobwereka ndalama.+