Yesaya 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu onse adzachotsedwa mʼdzikolo.Katundu yense wamʼdzikolo adzatengedwa,+Chifukwa Yehova ndi amene wanena mawu amenewa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:3 Yesaya 1, tsa. 261 Kukambitsirana, tsa. 357
3 Anthu onse adzachotsedwa mʼdzikolo.Katundu yense wamʼdzikolo adzatengedwa,+Chifukwa Yehova ndi amene wanena mawu amenewa.