Yesaya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+Chifukwa anyalanyalaza malamulo,+Asintha malamulo+Ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:5 Yesaya 1, ptsa. 261-263
5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+Chifukwa anyalanyalaza malamulo,+Asintha malamulo+Ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.*+