Yesaya 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vinyo watsopano akulira* ndipo mtengo wa mpesa wafota,+Anthu onse amene amasangalala mumtima mwawo akulira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:7 Yesaya 1, ptsa. 263-264
7 Vinyo watsopano akulira* ndipo mtengo wa mpesa wafota,+Anthu onse amene amasangalala mumtima mwawo akulira.+