Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:8 Yesaya 1, ptsa. 262, 264
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+