Yesaya 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo adzafuula mwamphamvu,Adzafuula mosangalala. Adzalengeza za ulemelero wa Yehova kuchokera kunyanja.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:14 Yesaya 1, ptsa. 264-266
14 Iwo adzafuula mwamphamvu,Adzafuula mosangalala. Adzalengeza za ulemelero wa Yehova kuchokera kunyanja.*+