Yesaya 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nʼchifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova mʼchigawo cha kuwala.*+Mʼzilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova, Mulungu wa Isiraeli.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:15 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 11 Yesaya 1, ptsa. 264-266
15 Nʼchifukwa chake iwo adzalemekeze Yehova mʼchigawo cha kuwala.*+Mʼzilumba zakunyanja adzalemekeza dzina la Yehova, Mulungu wa Isiraeli.+