Yesaya 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera mʼdzenje,Ndipo aliyense wotuluka mʼdzenjemo adzagwidwa mumsampha.+ Chifukwa zotsekera madzi akumwamba zidzatsegulidwa,Ndipo maziko a dziko adzagwedezeka. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:18 Yesaya 1, ptsa. 266, 267-268
18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera mʼdzenje,Ndipo aliyense wotuluka mʼdzenjemo adzagwidwa mumsampha.+ Chifukwa zotsekera madzi akumwamba zidzatsegulidwa,Ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.