Yesaya 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mwezi wathunthu udzachita manyazi,Ndipo dzuwa lowala lidzachita manyazi,+Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakhala Mfumu+ mʼphiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu,Ulemerelo wake waonekera pamaso pa achikulire a anthu ake.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:23 Yesaya 1, ptsa. 268-269, 270
23 Mwezi wathunthu udzachita manyazi,Ndipo dzuwa lowala lidzachita manyazi,+Chifukwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wakhala Mfumu+ mʼphiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu,Ulemerelo wake waonekera pamaso pa achikulire a anthu ake.*+