Yesaya 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu Yehova ndinu Mulungu wanga. Ndikukukwezani ndi kutamanda dzina lanuChifukwa mwachita zinthu zodabwitsa,+Zinthu zimene munali ndi cholinga choti muzichite kuyambira kalekale,+Mwazichita mokhulupirika+ komanso modalirika. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:1 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 141/15/1988, ptsa. 11-13 Yesaya 1, tsa. 271
25 Inu Yehova ndinu Mulungu wanga. Ndikukukwezani ndi kutamanda dzina lanuChifukwa mwachita zinthu zodabwitsa,+Zinthu zimene munali ndi cholinga choti muzichite kuyambira kalekale,+Mwazichita mokhulupirika+ komanso modalirika.