-
Yesaya 25:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Mwasandutsa mzinda kukhala mulu wamiyala
Tauni yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri mwaisandutsa bwinja lokhalokha.
Mzinda wachitetezo champhamvu wa anthu achilendo mwauthetsa
Ndipo sudzamangidwanso.
-