-
Yesaya 25:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mofanana ndi kutentha mʼdziko lopanda madzi,
Mumathetsa phokoso la anthu achilendo.
Mofanana ndi kutentha kumene kumatha kunja kukachita mitambo,
Nayonso nyimbo ya anthu ankhanza yaletsedwa.
-