-
Yesaya 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndipo mizinda yotetezeka yokhala ndi mipanda italiitali yolimba kwambiri,
Adzaigwetsera pansi.
Adzaigumula nʼkuigwetsera pansi, pafumbi penipeni.
-