Yesaya 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.* Chifukwa choti ndinu wowongoka mtima,Mudzasalaza njira ya anthu olungama. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:7 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 19
7 Njira ya munthu wolungama ndi yowongoka.* Chifukwa choti ndinu wowongoka mtima,Mudzasalaza njira ya anthu olungama.