Yesaya 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo. Iwo ndi akufa ndipo sadzaukanso.+ Chifukwa inu mwawapatsa chilangoKuti muwawononge nʼcholinga choti asadzatchulidwenso. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:14 Nsanja ya Olonda,3/1/2001, tsa. 20 Yesaya 1, tsa. 281
14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo. Iwo ndi akufa ndipo sadzaukanso.+ Chifukwa inu mwawapatsa chilangoKuti muwawononge nʼcholinga choti asadzatchulidwenso.