Yesaya 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova, pa nthawi ya mavuto iwo anatembenukira kwa inu kuti muwathandize.Mutawalanga, anakhuthulira mitima yawo kwa inu mʼpemphero lonongʼona.+
16 Inu Yehova, pa nthawi ya mavuto iwo anatembenukira kwa inu kuti muwathandize.Mutawalanga, anakhuthulira mitima yawo kwa inu mʼpemphero lonongʼona.+