-
Yesaya 26:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mofanana ndi mkazi woyembekezera amene watsala pangʼono kubereka,
Amene akulira chifukwa cha ululu wa pobereka,
Ndi mmenenso tikumvera chifukwa cha inu Yehova.
-