-
Yesaya 26:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ife tinali oyembekezera ndipo tinamva zowawa za pobereka,
Koma zili ngati tinabereka mphepo.
Sitinabweretse chipulumutso mʼdzikoli,
Ndipo palibe aliyense amene wabadwa kuti akhale mʼdzikoli.
-