Yesaya 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mudzalimbana naye ndi mfuu yoopseza pomuthamangitsa. Iye adzamuthamangitsa ndi mphepo yake yamphamvu pa tsiku lamphepo yakumʼmawa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:8 Yesaya 1, tsa. 285
8 Mudzalimbana naye ndi mfuu yoopseza pomuthamangitsa. Iye adzamuthamangitsa ndi mphepo yake yamphamvu pa tsiku lamphepo yakumʼmawa.+