-
Yesaya 28:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Komanso maluwa ake okongola amene akufota,
Amene avalidwa ndi mzinda umene uli paphiri, pamwamba pa chigwa chachonde,
Adzakhala ngati nkhuyu yoyambirira kucha chilimwe chisanafike.
Munthu akaiona, amaithyola nʼkuimeza mwamsanga.
-