Yesaya 28:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Izinso zachokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Amene zolinga zake ndi zabwino kwambiri,Ndipo zonse zimene amachita zimayenda bwino kwambiri.*+
29 Izinso zachokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,Amene zolinga zake ndi zabwino kwambiri,Ndipo zonse zimene amachita zimayenda bwino kwambiri.*+