Yesaya 29:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iweyo udzatsitsidwa,Uzidzalankhula uli pansi penipeni,Ndipo mawu ako azidzamveka otsika chifukwa cha fumbi. Mawu ako adzachokera mʼnthaka+Ngati mawu a munthu wolankhula ndi mizimu,Ndipo adzamveka ngati kulira kwa mbalame kuchokera mʼfumbi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:4 Yesaya 1, ptsa. 296-297
4 Iweyo udzatsitsidwa,Uzidzalankhula uli pansi penipeni,Ndipo mawu ako azidzamveka otsika chifukwa cha fumbi. Mawu ako adzachokera mʼnthaka+Ngati mawu a munthu wolankhula ndi mizimu,Ndipo adzamveka ngati kulira kwa mbalame kuchokera mʼfumbi.