Yesaya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tofa nato.+Iye watseka maso anu, amene ndi aneneri,+Ndipo waphimba mitu yanu, imene ndi anthu amasomphenya.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:10 Yesaya 1, ptsa. 298-299
10 Chifukwa Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tofa nato.+Iye watseka maso anu, amene ndi aneneri,+Ndipo waphimba mitu yanu, imene ndi anthu amasomphenya.+