Yesaya 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kwa inu masomphenya alionse akhala ngati mawu amʼbuku limene lamatidwa kuti lisatsegulidwe.+ Akalipereka kwa munthu wodziwa kuwerenga nʼkumuuza kuti: “Werenga bukuli mokweza,” iye adzanena kuti: “Sindingathe kuliwerenga, chifukwa ndi lomatidwa.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:11 Yesaya 1, ptsa. 298-299
11 Kwa inu masomphenya alionse akhala ngati mawu amʼbuku limene lamatidwa kuti lisatsegulidwe.+ Akalipereka kwa munthu wodziwa kuwerenga nʼkumuuza kuti: “Werenga bukuli mokweza,” iye adzanena kuti: “Sindingathe kuliwerenga, chifukwa ndi lomatidwa.”