Yesaya 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsoka kwa anthu amene amayesa kubisira Yehova mapulani awo oipa.*+ Zochita zawo amazichitira mumdima,Ndipo amati: “Ndi ndani akutiona? Ndi ndani akudziwa zimene tikuchita?”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:15 Yesaya 1, ptsa. 299-300
15 Tsoka kwa anthu amene amayesa kubisira Yehova mapulani awo oipa.*+ Zochita zawo amazichitira mumdima,Ndipo amati: “Ndi ndani akutiona? Ndi ndani akudziwa zimene tikuchita?”+