Yesaya 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene amanamizira anzawo mlandu,Amene amatchera misampha munthu amene akudziteteza* pa mlandu pageti lamzinda,+Ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni nʼcholinga choti asaweruze mwachilungamo mlandu wa munthu wolungama.+
21 Amene amanamizira anzawo mlandu,Amene amatchera misampha munthu amene akudziteteza* pa mlandu pageti lamzinda,+Ndiponso amene amagwiritsira ntchito mfundo zopanda umboni nʼcholinga choti asaweruze mwachilungamo mlandu wa munthu wolungama.+