Yesaya 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chifukwa akaona ana ake,Omwe ndi ntchito ya manja anga, ali naye limodzi,+Iwo adzayeretsa dzina langa.Inde, adzayeretsa Woyera wa Yakobo,Ndipo adzachita mantha ndi Mulungu wa Isiraeli.+
23 Chifukwa akaona ana ake,Omwe ndi ntchito ya manja anga, ali naye limodzi,+Iwo adzayeretsa dzina langa.Inde, adzayeretsa Woyera wa Yakobo,Ndipo adzachita mantha ndi Mulungu wa Isiraeli.+