Yesaya 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova wanena kuti: “Tsoka kwa ana aamuna osamvera,+Amene amachita zofuna zawo osati zofuna zanga,+Amene amapanga mgwirizano* koma osati motsogoleredwa ndi mzimu wanga,Kuti awonjezere tchimo pa tchimo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:1 Yesaya 1, tsa. 302
30 Yehova wanena kuti: “Tsoka kwa ana aamuna osamvera,+Amene amachita zofuna zawo osati zofuna zanga,+Amene amapanga mgwirizano* koma osati motsogoleredwa ndi mzimu wanga,Kuti awonjezere tchimo pa tchimo.