Yesaya 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amapita ku Iguputo+ asanandifunse,+Kuti akapeze chitetezo kwa Farao*Ndiponso kuti akabisale mumthunzi wa Iguputo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:2 Yesaya 1, ptsa. 302-303
2 Iwo amapita ku Iguputo+ asanandifunse,+Kuti akapeze chitetezo kwa Farao*Ndiponso kuti akabisale mumthunzi wa Iguputo.