Yesaya 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa akalonga ake ali ku Zowani,+Ndipo nthumwi zake zafika ku Hanesi.