Yesaya 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo adzachititsidwa manyaziNdi anthu amene sangawathandize chilichonse,Opanda phindu kapena ubwino uliwonse,Omwe ndi ochititsa manyazi ndi onyozetsa.”+
5 Iwo adzachititsidwa manyaziNdi anthu amene sangawathandize chilichonse,Opanda phindu kapena ubwino uliwonse,Omwe ndi ochititsa manyazi ndi onyozetsa.”+