Yesaya 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:7 Yesaya 1, ptsa. 303-304
7 Chifukwa thandizo lochokera ku Iguputo ndi losathandiza ngakhale pangʼono.+ Choncho iye ndamutchula kuti: “Rahabi+ amene amangokhala osachita chilichonse.”