-
Yesaya 30:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wogumuka kwa inu,
Ngati mpanda wautali umene wapendekeka ndipo watsala pangʼono kugwa.
Udzagwa mwadzidzidzi mʼkanthawi kochepa.
-