Yesaya 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Udzaphwanyika ngati mtsuko waukulu wadothi,Udzaphwanyikiratu wonse nʼkungokhala tizidutswatizidutswa ndipo patizidutswapo sipadzapezeka ngakhale phaleLoti nʼkupalira motoKapena kutungira madzi pachithaphwi.”* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:14 Yesaya 1, tsa. 307
14 Udzaphwanyika ngati mtsuko waukulu wadothi,Udzaphwanyikiratu wonse nʼkungokhala tizidutswatizidutswa ndipo patizidutswapo sipadzapezeka ngakhale phaleLoti nʼkupalira motoKapena kutungira madzi pachithaphwi.”*