Yesaya 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chifukwa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli, wanena kuti: “Mukabwerera kwa ine nʼkukhala odekha, mudzapulumuka.Mudzakhala amphamvu mukakhala odekha komanso mukasonyeza kuti mukundidalira.”+ Koma inu simunafune.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 11 Yesaya 1, tsa. 307
15 Chifukwa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli, wanena kuti: “Mukabwerera kwa ine nʼkukhala odekha, mudzapulumuka.Mudzakhala amphamvu mukakhala odekha komanso mukasonyeza kuti mukundidalira.”+ Koma inu simunafune.+
30:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2024, ptsa. 28-29 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 4 Nsanja ya Olonda,12/1/2006, tsa. 11 Yesaya 1, tsa. 307