Yesaya 30:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼmalomwake munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera mahatchi nʼkuthawa!” Choncho mudzathawadi. Munanenanso kuti: “Tidzakwera mahatchi othamanga kwambiri!”+ Choncho anthu amene adzakuthamangitseni adzakhala aliwiro kwambiri.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:16 Yesaya 1, ptsa. 307-308
16 Mʼmalomwake munanena kuti: “Ayi, ife tidzakwera mahatchi nʼkuthawa!” Choncho mudzathawadi. Munanenanso kuti: “Tidzakwera mahatchi othamanga kwambiri!”+ Choncho anthu amene adzakuthamangitseni adzakhala aliwiro kwambiri.+