Yesaya 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 11 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 232 Yesaya 1, ptsa. 311-312
23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+
30:23 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2022, tsa. 11 Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 232 Yesaya 1, ptsa. 311-312