-
Yesaya 30:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ngʼombe ndi abulu amene analima mundawo, zidzadya chakudya chokoma chosakaniza ndi zitsamba zowawasira, chimene mankhusu ake anauluzidwa pogwiritsa ntchito fosholo ndi chifoloko.
-