Yesaya 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa tsiku limene anthu ambiri adzaphedwe ndiponso nsanja zidzagwe, paphiri lililonse lalitali ndi paphiri lililonse lalingʼono padzakhala timitsinje ndi ngalande zamadzi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:25 Yesaya 1, ptsa. 311-313
25 Pa tsiku limene anthu ambiri adzaphedwe ndiponso nsanja zidzagwe, paphiri lililonse lalitali ndi paphiri lililonse lalingʼono padzakhala timitsinje ndi ngalande zamadzi.+