Yesaya 30:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali.Likubwera ndi mkwiyo wake woyaka moto ndiponso mitambo yolemera. Iye akulankhula mwaukali,Ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:27 Yesaya 1, ptsa. 312-313
27 Taonani! Dzina la Yehova likubwera kuchokera kutali.Likubwera ndi mkwiyo wake woyaka moto ndiponso mitambo yolemera. Iye akulankhula mwaukali,Ndipo lilime lake lili ngati moto wowononga.+